Buku Lopatulika 1992

Zekariya 12:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsiku ilo Yehova adzacinjiriza okhala m'Yerusalemu; ndi iye wokhumudwa pakati pao tsiku lomwelo adzakhala ngati Davide; ndi nyumba ya Davide idzakhala ngati Mulungu, ngati mthenga wa Yehova pakati pao.

Zekariya 12

Zekariya 12:1-12