Buku Lopatulika 1992

Zefaniya 1:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzacitika nthawi yomweyi kuti ndidzasanthula Yerusalemu ndi nyali, ndipo ndidzalanga amunawo okhala ndi nsenga, onena m'mtima mwao, Yehova sacita cokoma, kapena kucita coipa.

Zefaniya 1

Zefaniya 1:10-14