Buku Lopatulika 1992

Yuda 1:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ndifuna kukukumbutsani mungakhale munadziwa zonse kale kuti Ambuye, atapulumutsa mtundu wa anthu ndi kuwaturutsa m'dziko La Aigupto, anaononganso iwo osakhulunirira.

Yuda 1

Yuda 1:1-6