Buku Lopatulika 1992

Yoswa 8:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Yehova anati kwa Yoswa, Tambasula nthungo iri m'dzanja lako iloze ku Ai, pakuti ndidzaupereka m'dzanja lako. Ndipo Yoswa anatambasula nthungoyo inali m'dzanja lace kuloza mudzi.

Yoswa 8

Yoswa 8:11-22