Buku Lopatulika 1992

Yoswa 18:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo malire ao a kumpoto anacokera ku Yordano; ndi malire anakwera ku mbali ya Yeriko kumpoto, nakwera pakati pa mapiri kumadzulo; ndi maturukiro ace anali ku cipululu ca Beti-aveni.

Yoswa 18

Yoswa 18:10-19