Buku Lopatulika 1992

Yona 3:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mulungu anaona nchito zao, kuti anabwera kuleka njira yao yoipa; ndipo Mulungu analeka coipa adanenaci kuti adzawacitira, osacicita.

Yona 3

Yona 3:1-10