Buku Lopatulika 1992

Yona 2:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti munandiponya mwakuya m'kati mwa nyanja,Ndipo madzi anandizinga;Mapfunde anu onse a nyondonyondo anandimiza.

Yona 2

Yona 2:1-10