Buku Lopatulika 1992

Yona 2:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati,Ndinaitana Yehova m'nsautso yanga,Ndipo anandiyankha ine;Ndinapfuula ndiri m'mimba ya manda,Ndipo munamva mau anga.

Yona 2

Yona 2:1-10