Buku Lopatulika 1992

Yona 1:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo amunawo anaopa kwambiri, nati kwa iye, Ici nciani wacicita? Pakuti amunawo anadziwa kuti anathawa pamaso pa Yehova, popeza adawauza.

Yona 1

Yona 1:1-16