Buku Lopatulika 1992

Yeremiya 35:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ndinawalowetsa m'nyumba ya Yehova, m'cipinda ca ana a Hanani mwana wa Igadaliya, munthu wa Mulungu, cokhala pambali pa cipinda ca akuru, ndico cosanjika pa cipinda ca Maseya mwana wa Salumu, mdindo wa pakhomo;

Yeremiya 35

Yeremiya 35:1-7