Buku Lopatulika 1992

Oweruza 3:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

anasiya mafumu asanu a Afilisti ndi Akanani onse, ndi Asidoni, ndi Ahivi okhala m'phiri la Lebano, kuyambira phiri la Baalaherimoni mpaka polowera ku Hamati.

Oweruza 3

Oweruza 3:1-5