Buku Lopatulika 1992

Obadiya 1:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

MASOMPHENYA a Obadiya. Atero Ambuye Yehova za Edomu: Tamva mbiri yocokera kwa Yehova, ndi mthenga wotumidwa mwa amitundu, ndi kuti, Nyamukani, timuukire kumthira nkhondo.

Obadiya 1

Obadiya 1:1-10