Buku Lopatulika 1992

Nyimbo 8:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndaniyu acokera kucipululu,Alikutsamira bwenzi lace?Pa tsinde la muula ndinakugalamutsa mnyamatawe:Pomwepo amako anali mkusauka nawe,Pomwepo wakukubala anali m'pakati pa iwe.

Nyimbo 8

Nyimbo 8:1-9