Buku Lopatulika 1992

Nyimbo 5:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndinamtsegulira bwenzi langalo;Koma ndinampeza, bwenzi langa atacoka.Moyo wanga unalefuka polankhula iye:Ndinamfunafuna, osampeza;Ndinamuitana, koma sanandibvomera.

Nyimbo 5

Nyimbo 5:1-16