Buku Lopatulika 1992

Nehemiya 2:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinakwera usiku kumtsinje, ndi kuyang'ana lingali; ndinabwerera tsono ndi kulowa pa cipata ca kucigwa, momwemo ndinabwereranso.

Nehemiya 2

Nehemiya 2:10-20