Buku Lopatulika 1992

Maliro 1:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Udio wace unali m'nsaru zace; sunakumbukira citsiriziro cace;Cifukwa cace watsika mozizwitsa; ulibe wakuutonthoza;Taonani Yehova, msauko wanga, pakuti mdaniyo wadzikuzayekha.

Maliro 1

Maliro 1:1-12