Buku Lopatulika 1992

Maliro 1:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anthu ace onse ausa moyo nafunafuna mkate;Ndi zokondweretsa zao agula zakudya kuti atsitsimutse moyo wao;Taonani, Yehova, nimupenye; pakuti ndasanduka wonyansa.

Maliro 1

Maliro 1:8-14