Buku Lopatulika 1992

Malaki 2:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kodi sitiri naye Atate mmodzi ife tonse? sanatilenga kodi Mulungu mmodzi? Ticita monyengezana yense ndi mnzace cifukwa ninji, ndi kuipsa cipangano ca makolo athu?

Malaki 2

Malaki 2:3-15