Buku Lopatulika 1992

Luka 13:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nthawi yomweyo anadzapo Afarisi ena, nanena kwa iye, Turukani, cokani kuno; cifukwa Herode afuna kupha lou.

Luka 13

Luka 13:29-34