Buku Lopatulika 1992

Levitiko 6:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Copereka ca Aroni ndi ana ace, cimene azibwera naco kwa Yehova tsiku la kudzozedwa iye ndi ici: limodzi la magawo khumi la efa la ufa wosalala, likhale copereka caufa kosalekeza, nusu lace m'mawa, nusu lace madzulo.

Levitiko 6

Levitiko 6:13-26