Buku Lopatulika 1992

Levitiko 20:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Potero musiyanitse pakati pa nyama zoyera ndi nyama zodetsa, ndi pakati pa mbalame zodetsa ndi zoyera; ndipo musadzinyansitsa ndi nyama, kapena mbalame, kapena ndi kanthu kali konse kakukwawa pansi, kamene ndinakusiyanitsirani kakhale kodetsa.

Levitiko 20

Levitiko 20:20-27