Buku Lopatulika 1992

Eksodo 39:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi mpango wa efodi wokhala pamenepo, wakummanga nao unali woombera kumodzi wa ciombedwe comweci; wa golidi, ndi lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira, ndi bafuta wa thonje losansitsa; monga Yehova adauza Mose.

Eksodo 39

Eksodo 39:1-15