Buku Lopatulika 1992

Eksodo 37:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anapanga coikapo nyali ca golidi woona; mapangidwe ace a coikapo nyalico anacita cosula, tsinde lace ndi thupi lace, zikho zace, mitu yace, ndi maluwa ace zinakhala zocokera m'mwemo;

Eksodo 37

Eksodo 37:14-22