Buku Lopatulika 1992

Deuteronomo 17:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ukakulakani mlandu pouweruza, ndiwo wakunena zamwazi, kapena zakutsutsana, kapena zakupandana, ndiyo mirandu yakutengana m'midzi mwanu; pamenepo muziuka ndi kukwera kumka ku malo amene Yehova Mulungu wanu adzasankha;

Deuteronomo 17

Deuteronomo 17:6-13