Buku Lopatulika 1992

Amosi 4:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti taona, Iye amene aumba mapiri, nalenga mphepo, nafotokozera munthu maganizo ace, nasanduliza m'mawa ukhale mdima, naponda pa misanje ya dziko lapansi, dzina lace ndiye Yehova Mulungu wamakamu.

Amosi 4

Amosi 4:12-13