Buku Lopatulika 1992

Aefeso 5:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo yendani m'cikondi monganso Kristu anakukondani inu, nadzipereka yekha m'malo mwathu, copereka ndi nsembe kwa Mulungu, ikhale pfungo lonunkhira bwino.

Aefeso 5

Aefeso 5:1-6