Buku Lopatulika 1992

2 Samueli 7:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pakuti sindinakhala m'nyumba kuyambira tsiku lija ndinaturutsa ana a Israyeli ku Aigupto kufikira lero lomwe, kama ndinayenda m'cihema ndi m'nyumba wamba.

2 Samueli 7

2 Samueli 7:3-13