Buku Lopatulika 1992

2 Samueli 11:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene anauza Davide kuti, Uriya sanatsildra ku nyumba yace, Davide ananena ndi Uriya, Kodi sunabwera kuulendo? cifukwa ninji sunatsikira ku nyumba yako?

2 Samueli 11

2 Samueli 11:1-12