Buku Lopatulika 1992

2 Samueli 10:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma akalonga a ana a Amoni anati kwa Hanuni mbuye wao, Kodi muganiza kuti Davide alemekeza atate wanu, popeza anakutumizirani osangalatsa? Kodi Davide sanatumiza anyamata ace kwa inu, kuti ayang'ane mudziwo ndi kuuzonda ndi kuupasula?

2 Samueli 10

2 Samueli 10:1-7