Buku Lopatulika 1992

2 Mbiri 14:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi Asa ndi anthu anali naye anawalondola mpaka ku Gerari, nagwa Akusi ambiri osalimbikanso mphamvu iwowa; pakuti anathyoledwa pamaso pa Yehova ndi ankhondo ace; ndipo anatenga zofunkha zambiri.

2 Mbiri 14

2 Mbiri 14:4-14