Buku Lopatulika 1992

2 Mbiri 1:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu inatero kuti siliva ndi golidi zikhale m'Yerusalemu ngati miyala, ndi kuti mikungudza icuruke ngati mikuyu yokhala kucidikha.

2 Mbiri 1

2 Mbiri 1:11-17