Buku Lopatulika 1992

2 Mafumu 5:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace khate la Namani lidzakumamatira iwe ndi mbumba yako cikhalire. Ndipo anaturuka pamaso pace wakhate wa mbu ngati cipale cofewa.

2 Mafumu 5

2 Mafumu 5:19-27