Buku Lopatulika 1992

2 Atesalonika 1:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kukatero tikupemphereraninso nthawi zonse, kuti Mulungu wathu akakuyeseni inu oyenera kuitanidwa kwanu, nakakwaniritse comkomera conse, ndi nchito ya cikhulupiriro mumphamvu;

2 Atesalonika 1

2 Atesalonika 1:10-12