Buku Lopatulika 1992

2 Akorinto 4:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti zonsezi nza kwa inu, kuti cisomoco, cocurukitsidwa mwa unyinjiwo, cicurukitsire ciyamiko ku ulemerero wa Mulungu.

2 Akorinto 4

2 Akorinto 4:10-18