Buku Lopatulika 1992

1 Timoteo 4:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munthu asapeputse ubwana wako; komatu khala citsanzo kwa iwo okhulupira, m'mau, m'mayendedwe, m'cikondi, m'cikhulupiriro, m'kuyera mtima.

1 Timoteo 4

1 Timoteo 4:7-16