Buku Lopatulika 1992

1 Petro 5:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mwa Silvano, mbale wathu wokhulupirika monga ndimayesa, ndalembera kwa inu mwacidule, ndi kudandaulira, ndi kucita umboni, kuti cisomo coona ca Mulungu ndi ici; m'cimeneci muimemo.

1 Petro 5

1 Petro 5:10-14