Buku Lopatulika 1992

1 Akorinto 7:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace ndiyesa kuti ici ndi cokoma cifukwa ca cibvuto ca nyengo yino, kuti nkwabwino kwa munthu kukhala monga ali.

1 Akorinto 7

1 Akorinto 7:25-32