Buku Lopatulika 1992

1 Akorinto 7:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma kunena za anamwali, ndiribe lamulo la Ambuye; koma ndikuuzani coyesa ine, monga wolandira cifundo kwa Ambuye kukhala wokhulupirika.

1 Akorinto 7

1 Akorinto 7:19-29