Buku Lopatulika 1992

1 Akorinto 5:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kwamveka ndithu kuti kuli cigololo pakati pa inu, ndipo cigololo cotere conga sicimveka mwa amitundu, kuti wina ali naye mkazi wa atate wace.

1 Akorinto 5

1 Akorinto 5:1-4